Za Ife
16/02/2026
Panali kusamvana pakati pa asilikari a MDF komanso apolisi ku Zomba.
(Video kuma comment)
Tapeza kuti msilikari wina waudindo anamangidwa ndi apolisiwa kamba koyendetsa galimoto yake ataledzera koma izi sizinasangalatse asilikari ena omwe anapita malo amene apolisiwa amachita chipikisheni magalimoto kukabweza chipongwe.
Kanemayu akuonetsa apolisiwa atagwaditsidwa kwinaku akuuzidwa kuti apepese.
27/01/2026
President waku Uganda Yoweri Museveni akumayenda mu chi Glass kwachuluka adani kuopa kumuombera
atelo ATI nkuntchisi tu kumeneko anthu akuyenda mmi nseu ya golide
😃😃
13/01/2026
Madness Entertainment yati yasayina chinanso. Uyu ndi Nava Madness, mwana wa dzaka 21 yemwe Madness yalengeza kuti watengedwa kukhala modzi wa oyimba wawo.
Congratulations and all the best Nava 👏
khangati uyu ndi replacement yawina uja 😂
akati ng'onA 😂
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Africa
Kampala