YONECO FM

YONECO FM

Share

10/07/2026

Zomba City Council says it is yet to access its allocation of funds for project preparation under the reformed Constituency Development Fund (CDF).

The Ministry of Finance recently announced the release of K7.8 billion in CDF allocations to local councils, with disbursements made only to councils that submitted the required work plans and project documentation.

Speaking to YFM, Zomba City Council Public Relations Officer Aubrey Moses said the council has received official communication from the Ministry of Finance regarding the funds but has not yet received the allocation.

Moses said the council has fulfilled all the required conditions, including the submission of work plans and project documentation, and has no outstanding issues.

By Temwa Tembo

10/07/2026

Bwalo la milandu munzinda wa Blantyre, lero likupitiliza kumva mulandu okhudza anthu asanu ndi awiri omwe akuganiziridwa kuti anapha dotolo wa pachipatala cha Queen Elizabeth, a Victoria Bobe, powawombera ndi mfuti kunyumba kwawo ku Chigumula.

Mulanduwu unayimitsidwa lachitatu lapitali pomwe mboni yachitatu yomwenso ndi m’modzi mwa apolisi kunthambi ya zakafukufuku kuchigawo chakummwera a Christopher Pangeti anaperekera umboni wawo.

Patsikuli, ngati mbali imodzi ya umboni wa a Pangeti, bwalori linawonetsedwa kanema yemwe anajambulidwa ndi apolisi kunyumba kwa malemu Dr. Bobe kuwonesetsa oganiziridwawa akulongosola mmene anapangira chiwembuchi.

Oweruza mulandu a Ruth Chinangwa, anayimisa mulanduwu pofuna kupereka mpata kuti zomwe zinawoneredwa pa kanemazi zilembedwe.

Kum’mawa kuno, oyimira mbali ya oganiziridwa pa mulanduwu, a Michael Goba Chipeta, akuyembekezeka kufunsa mafunso a Pangeti.

Wolemba Smart Sochela (Blantyre)

Want your business to be the top-listed Media Company in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Youth Net & Counselling (YONECO)
Zomba
471