Laugh With Geoffrey
24/07/2023
Not a matter to laugh about π₯Ίπ share the post let's be part of the help as our friend is stranded π₯ΊππΎ
Pomwe vuto lakusowa ntchito likadali lalikulu pakati pa mzika zochuluka maka achinyamata, wachinyamata wina waima pafupi ndi chipata cha likulu la ofesi zaboma ku Lilongwe atanyamula pepala lomwe walembapo kuti akufuna ntchito yoyendetsa galimoto.
Izi zimachitika kwambiri mmaiko omwe ndi otukuka.
by Cassim Aubi
15/07/2023
KUIPHULA KOSAYEMBEKEZEREKA.
Lethukukhanya ndi mwana wamkazi wa zaka zitatu zakubadwa wa m'dziko la South Africa amene wagwedeza mma social media kuyambira dzana.
Mwanayu makolo ake anamutuma kugolosale masiku apitawa kukagula bread ndipo pochokera kumeneko anaima pa zithaphwi za madzi n'kumasewera ndi madziwo uku bread uja ali mmanja.Photographer anamujambula mwanayo zithunzi pa chithaphwipo zomwe zinayamba kuyenda mma social media.
Zithunzizo zinapereka chidwi kwa anthu ochuluka maka chifukwa cha mtsangala ya mwanayo komanso nkhope yake yachimwemwe.Zithunzizo zitayenda mma social media zidakafika ku company yopanga bread yo yomwe inapita kwa makolo a mwanayo kukawapempha kuti mwanayo akhale pa billboard atanyamula bread yo ngati advert komanso akhale ambassador wa bread yo.
KUIPHULA KOSAYEMBEKEZEREKA.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Zomba