Titukulane RFSA

Titukulane RFSA

Share

Photos from Titukulane RFSA's post 04/12/2024

Lero ndi tsiku lachiwiri pa msonkhano omaliza okambirana zomwe pulojekiti ya Titukulane yachita mu zaka zisanu.... Dzulo anthu akuluakulu angapo analankhulapo pa momwe pulojekitiyi yayendera ndi zinthu zomwe zakhazikika pakati pa anthu omwe apindula ndi pulojekitiyi kuphatikizapo Wachiwiri wa Mtsogoleri wa dziko lino. Lero anthu alawira m'mawa, kupitiriza zokambiranazi zomwe zimalizike lero.

02/12/2024

Tsiku lijatu ndi mawa.... Pomwe mwambo wa masiku awiri okondwelera zonse zimene taphunzira ndi kupindulapo mu ntchito za Titukulane ukutseguliridwa! Kumeneko kukakhala zionetsero komanso kwakulukulu, kulankhulapo momwe ntchito ya Titukulane yakwanitsira kutukula miyoyo ya anthu a ku Mangochi ndi ku Zomba. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Olemekezeka Dr Michael Usi ndiye akakhale mlendo olemekezeka pa mwambowu. Pomwe pulojekiti ya Titukulane ikupita ku mapeto, inu muzayikumbukira bwanji kumeneko?

Photos from CARE Malawi's post 25/07/2024
Want your organization to be the top-listed Non Profit Organization in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Mayfair Office Park
Zomba

Opening Hours

Monday 07:30 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:30 - 17:00
Friday 07:30 - 13:30