UNCLE KHIRI
05/04/2025
Iyi ndi nkhani ya mayi Magret Chimwaza omwe amachokera mu mzinda wa zomba. mayiwa ali ndi zaka 77. ndipo kamba kamavuto azachuma amapemphesa ntauniyi. amasaka ntchito koma anthu amawakana kuti ndi achikulire sangakwanitse kugwila ntchito iliyonse. onera kufotokoza za momwe anayambira kupemphesa. also follow UNCLE KHIRI for more updates. watch the video here
Anayamba Bwanji Kupemphesa Mayi Magret Chimwaza aKu zomba Iyi ndi nkhani ya mayi Magret Chimwaza omwe amapemphesa Ntownship ya zomba, mayiwa ndi achikulire ndipo ali ndi zaka 77, mayiwa amakanidwa ntchito chifukwa c...
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Chinamwali
Zomba
265881768837