Chipini News-Updates
Anthu olusa atentha nyumba kwa Kamoto
Anthu okwiya ammudzi mwa Kamoto atentha nyumba ya nkulu wina opanga business pa Kamoto pafupi ndi Nansambo school. Bambo dzina lao ndi Akholio izi zachitika kamba koganiziridwa kuti anali m'gulu limene linasowetsa bambo Ena otchedwa Bambo Chafudzika. Bambo Chafudzika anamwalira mwezi wa January ndipo anauka myezi iwiri yapitayi koma nkhope itasinthidwa...Chipini News yapeza zimenezo padakali pano Zina zikamveka tikupatsirani
15/07/2022
Zomba Chingale MP motivates secondary school girls to work hard
Member of Parliament for Zomba Chingale, Lonnie Phiri, has called on secondary schools girls in her constituency to work hard and aspire to be in top positions in future instead of getting married at the expense of education.
Read more at: https://malawi24.com/2022/07/15/zomba-chingale-mp-motivates-secondary-school-girls-to-work-hard/
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Zomba