Rock Visuals
22/05/2026
π *2026 Graduation Season is Here!*π
Kwa onse omaliza maphunziro awo a Form 4 m'masukulu a ku Mulanje β nthawi yakwana yojambula zithunzi zokongola za Graduationyanu!
Rock Visuals ikukupatsani mwayi wosaiwalika wa:
- Professional Graduation Portraits
- Group & Family Photos
- Cap & Gown Sessions
- HD Photos ndi Videos
M'masukulu awa:
- Chinyama CDSS
- Satemwa CDSS
- Dzenje Secondary School
- Seed Of Hope PVT Secondary School
- Salabango CDSS
- Nansomba Secondary School
- Mendulo CDSS
-Chikhwaza Secondary School ndi ena ambiri
Mukufuna kujambulitsa tsiku lanu lapadera? Timabwera ku school yanu nkuzajambula . Booking ikuyamba tsopano
π WhatsApp or Call: 0993555131
π Along M2 Road, Chinakanaka Trading Centre, Mulanje
Tag mzanga, mlongo, kapena mwana wanu omwe akumaliza Form 4 m'chaka chino π
Letβs make your graduation memories legendary! β¨
18/05/2026
Ndi chifukwa chiyani Rock Visuals ndi yabwino kwambiri?
1. Zithunzi za HD quality zenizeni
2. Editing yabwino kwambiri yomwe imakupangitsani kuwala
3. Timabwera komwe muli (Mulanje, Thyolo, Zomba, Chiradzulu, Blantyre, Chikwawa, Nsanje, Villa Milange)
4. Mtengo wabwino: K3000 per HD photo
Mukufuna ma pictures a Birthday, Engagement, Family, kapena Music Video?
Inbox or call/WhatsApp 0993555131 tsopano!
Rock Visuals - Where moments become legends π₯
30/04/2026
HAPPY BIRTHDAY to our amazing young Client, Collinsπ! πΈ
Want to make your birthday unforgettable? Book a photoshoot at Rock Visuals Studio and let's create some epic memories π!
π Call us 0993555131
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Mulanje M2
Mulanje
Opening Hours
| Monday | 07:00 - 18:00 |
| Tuesday | 07:00 - 18:00 |
| Wednesday | 07:00 - 18:00 |
| Thursday | 07:00 - 18:00 |
| Friday | 07:00 - 18:00 |
| Saturday | 07:00 - 18:00 |
| Sunday | 07:00 - 18:00 |