MATW-KBz
Hie guyz
Zizakhala za bwino tizacheza ngat pano ena inu ndiazanthu koma pasi pa phasa mukusunga lupanga lokuthwa.......pot zdalembedwa masiku osiliza tiyenela kuvasa...matw-kbz kwa ena ife mwna mawuwa ndi achilendo eee ife ndi khuluu yomwe imakhala ikumwaza uthanga kuzela mumayimbidwe zizakhala zosangalasa titapeza sposa yotithandiza kwa amene akufuna kwa bwino atelo atha kuimba pa number aw 0990742953 kapena 0888834679 m***a kutipeza pamanambala amenewa,ife luso tili nawo Koma Khan nd ndalama...zabwibo zose kwa amene akufuna kuthandiza..osaila kupanga like pa pageyi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mutwika Village
Mulanje