DON TARZ
Ine ndinabadwa wamanyazi, manyazi ndikuti manyazi... ๐ถ๐ถ๐ต๐ถ
13/06/2026
Ma DRINKS A AKULU A MPINGO PA LAKERS โตโต
Every show is a blessing.๐๐พโค๏ธ
Pa Waliranji Depot ku Mchinji pali spot ya bho ya ma show pa ๐คโ
Last night we had an amazing time with the Akumudzi Band. The love, energy and support from the fans super super ๐๐ GOOD VIBES ๐ค๐ธ๐ถ
Oimba ndi ma band, tiyeni tizikonzanso ma events mma districts ndi mma trading centres. Anthu akumeneko amafunanso good vibes, it gives fans a chance to Watch their favorite artists and Bands performing Live and Direct. ๐ฅ Kuli ma fans oti kukuona ndikumatsutsa kuti iweyo si iweyo๐๐ coz amangokuona mma HD pictures and videos utadzijudula zooonjeza utakwera magalimoto obwerekawa๐๐๏ธ๐คฃ๐คฃ
will always be there, but sometimes we have to sacrifice for the fans on the other side osati ma show onse mma city mokha mokha. Kuli ma Loyal fans mmidzimu omaimba nawo nyimbo lyric by lyric kuchokera pa intro mpaka kumapeto kwa song. That love deserves recognition. โค๏ธ
Big love and respect to all the fans dem. ๐๐พLakers Side we give thanks always. ๐ฏ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Address
Lilongwe