InfoNow
21/04/2026
Rodrick who? Gonani kaye mwatopa 😀
A drop in food prices is relief, but a surge in energy prices is a reminder that the cost of living remains high. 😴
03/04/2026
Mnyengo ngati yomweyi mu 2002 maule FCB Nyasa Big Bullets anamenya game ndi noma Mighty Wanderers FC mtima uli ku bash yomwe Carlsberg inkachititsa ku Mangochi. Bash inayamba Easter Friday ndipo game inkamenyedwa pa Easter Saturday pa Kamuzu Stadium ku Blantyre.
Game yi inali Charity match ndipo anakonza anali a Women in Business ngati Fundraising. Inali game ya ma temper moti Peter "mjojo" Mponda anapatsidwa Red card. Izi zinapangitsa ma palestina kuopseza referee kuti amukang'antha zomwenso zinapangitsa kuti mpira uyimitsidwe kwa mphindi 30.
Pakutha pa 90 minutes game inathela 1 (Fisher Kondowe) - 1 (Andrew Chikhosi) ndipo bullets sinadikilenso za extra time kapena ma penalty kuti papezeke owina ngakhale zinali zofunika kutero popeza ankaona kuchedwa komanso anangomenyera umodzi omwewo.
Ku bash Captain Jones "speed link" Nkhwazi mothandizana ndi Kumbukani "banya" Lungu anakabandulana ndi ma DJ pandewu yomwe anaiputa Grant "ginte" Lungu atasemphana ndi osakaniza saundiwa.Mwina sankaika saundi yabwino 😀. Tidikila a ginte atiyankhule 😅.
"Happy Easter" Maule ndi Nyerere.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lilongwe