Simon Peter
10/06/2026
On this day 10 June 2024 chisoni chachikulu chinakuta dziko la Malawi ...zimkawoneka ngati tikulota ..koma ayi ndithu
1. His Honour Dr. Saulos Klaus Chilima
2. Major Flora Selemani Ngwirinji
3. Mr. Lukas Kapheni
4. Mr. Chisomo Chimaneni
5. Ms. Gloria Mtukule
6. Ms.Shanil Dzimbiri
7. Mr. Dan Kanyemba
8. Mr. Abdul Kingstone Lapukeni
9. Colonel Sambalopa.
05/06/2026
Brother in the Lord Judas Iscariot wayamba Business yoweta timbalame ...let's support our Brother
10500...akumatumiza kulikonse komwe mungafune
28/05/2026
Meeting ya azitumiki aMulungu
Malumbo Ngaiyaye wayamba kubela anthu ndalama mudzina la Chakhumi ..nde ndinaganiza zomuyendela kuti timuuze kuti asiyiletu mchitidwe wakusaweluzika wu.
Koma Malomwake ndaona kuti naneso ndiyambe kulandila Chakhumi molowa m'manja
Ndalama alinazo koma Swagger sangamake
26/05/2026
Zeze pamodzi ndi ine Simon Peter tikuti Happy Birthday to The Kingstons MW Doro - Simon - Zeze
Uyu ndi Age met wathu ... Simon Peter 52 yrs. ZeZe 45 yrs Our Queen 👑 Dorothy 32 yrs
Wa Mkulu ndiMulungu anthu timangosiyana tsiku komaso chaka chobadwila ena amabadwa changu onena mochedwelapo
Uyu amapeleka molowa mmanja ku Church kwanthu
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe