YOUTH ALERT
Eti kupanga force relationship, nayonso ndi labour?
Anyway, Happy Labour Day kachikena.
01/05/2026
Happy International Labour Day
Achinyamata, ntchito si ndalama zokha — Ma Brainwaves amafunika kukhala ali nyatwa! 🧠💚
Kodi workplace anu ali sharp sharp… or “healthy environment” is just a theory basi? 🤔
Madolo its a YA! Podcast Time
“It’s just a comment… or is it?” 💻🔥
What starts as a joke in the comments can turn into real damage.
Cyberbullying is louder than we think—and closer than we admit.
Episode iyiyi. George & Tadz discuss Cyberbullying
👀 Have you ever been targeted… or stayed quiet while it happened?
Hello guys..
So nzathu wina wake wativungila funso ku DM kwathu, funsoli nali: why have we young people normalized having s*x now than before? Why is s*x common.?
21/04/2026
Happy World Creativity and Innovation Day! 🎨✨
Lero pa World Creativity and Innovation Day tikukumbutsa tokha kuti creativity si ya ma artist okha ayi — aliyense ali ndi mphamvu yopanga ma ideas atsopano. Kaya ndi pa hustle yanu, bizinesi, sukulu kapena pa moyo watsiku ndi tsiku — thinking differently is power.
Nthawi zina timaganiza kuti “zilipo kale,” koma innovation imayambira pa ma small ideas amene timanyalanyaza. Maybe idea yanu ingasinthe community yanu kapena ngakhale dziko lonse 🌍
Tell us in the comments — ndi idea yanji yomwe muli nayo koma simunayambe kugwira ntchito nayo? kapena what’s one creative thing you’ve done recently?
Let’s inspire each other 💡
Click here to claim your Sponsored Listing.
Contact the business
Telephone
Website
Address
Family Health Services (FHS)/
Lilongwe