ENI MUDZI

ENI MUDZI

Share

01/09/2025

Congratulations 🎉 Rashley Pamene Nyimbo yake ya LAKWILA yakwanitsa 200k Views in 8days Yomwe Ndi improvement yake yayikulu Kwambili 🤝

01/09/2025

Eni Mudzi ayambisa Kale ndewu Kunoo 😂eeeh

01/09/2025

This is the Most Booked Artist Right Now Zeze Kingston 👑..

31/08/2025

Zeze Afuna apangise Show yaulele Ku Brantley ndipo Azimba Zeze Ndi Jetu ...starting 11AM

31/08/2025

Alert MSCE yamalizidwa Kuchongedwa Ndipo Zikunveka Kuti Ma Results Atulutsidwa Friday Likubwelali Nde please Kumayenda Mutadya Kumeneko ...Maneb will shortly Confirm the date...

31/08/2025

Congratulations FADA MOTI Pamene Nyimbo yake Yomwe inamupangisa Kuziwika Ku N'tundu Kwa Malawi Called " Mudyela" yakwanitsa 1milion Views ......A FADA MWABWELA🤝

31/08/2025

Agogowa nde ABEBA ku TikTok Zuonesa Ayiphula Ndipo Ena akuti angokwatilana Ndi Jetu...

31/08/2025

From Inbox Munthu Wina watipeza ati watola Ndalama Ndipo Ngati Pali amene angakwanitse Kunena Amount ya ndalamayi Ndipomwe anataya Akupasa Ndipo akhala akuwelenga Ma Comment....

31/08/2025

Kodi A Rashley Chisangalalo Chokhachokhachi Ichi??? Mpka Zende inuo??

31/08/2025

Amidu wadandaula Zomamujambula Akamaipota Nsima kwawo..Izizi sizabwino Gys Kapena aziphikila Ku Chipinda???

31/08/2025

🤧

31/08/2025

Ana Amene alemba Mayeso awo A form 4 Chaka chino akufunisisa Kuti Mayeso awo atuluke Relo Mwachangu Pachifukwa Cha Kusitha Kwa syllabus Class yolemba Mayeso Mu form 4 ikhala imene ikulemba MSCE 2026 ..The rest azalemba MSCE mu form 6 Kamba ka Kusitha Kwa syllabus ..Zomwe Zikhale zowawa Kwa Omwe sachita Bwino Nde Ndichifukwa ana ambili akufunisisa Kuti Ma results atuluke Relo...

Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Culinary Team

Attire

Telephone

Website

Address


Lilongwe