BACK DAYS Pictures
17/01/2026
Kumpando,
Anthu amu Lilongwe ndi msika wanji uwu?
First Pic : Normal Camera
Second Pic: After Raja
Inu mwakwera iti? Normal or Raja?😂
Kumpando,
Enafe tili ngat ma 4n ovuta ku charger... moyo wathu umafunika madalitso amphamvu osakaniza ndi mapemphero a abale
Tikufunika ma fast charger kuti zathu ziyende...komano ma 4n ovuta ku charger pena amavutaso ku charger olo utaika fast charger ngat pali izi:
voltage
connection with the charger
charging base
So for your life to charge fast, make sure there is No LOW VOLTAGE OF PRAYERS, BETTER CONNECTION WITH YOUR GOD AND GREAT CHARGING BAS
Zizayenda.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe