LILONGWE CCAP

LILONGWE CCAP

Share

17/05/2026

CHICHEWA SERVICE
TSIKU:17 May 2026

06/05/2026

Lero Abusa DF Zembeni omwe ndi m'busa wa Lilongwe CCAP komanso Abusa ena anali limodzi ndi Mlaliki , Reine Coetzee, wochokera ku Cape Town m’dziko la South Africa,yemwe ali mdziko muno paulendo wake wapadera woyenda wapansi kupita ku Israel, atanyamula mtanda ngati chizindikiro cholalikira uthenga wa chipulumutso cha Yesu Khristu.

Iye adayamba ulendowu pa 16 March chaka chatha ku South Africa, ndipo mpaka pano wakwanitsa kuyenda makilomita okwana 3,382 wapansi. Pa ulendowu wadutsa m'maiko monga Mozambique ndi Zimbabwe, ndipo pakali pano akupita ku Tanzania.

Want your place of worship to be the top-listed Place Of Worship in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


M1 Road
Lilongwe