Comm vee uja

Comm vee uja

Share

29/11/2024

👩‍🦰Girl : Chatha
🧒 Boy :Okay
👩‍🦰Girl : Basi Kodi?
🧒 Boy : Umafuna Nditseke Ndi Pemphero?
😂😂🤓🏃‍♀️🤣🤣

08/12/2022

Usiku wabwino anthu anga

21/11/2022

Muli bwanji a Malawi konse komwe muli?

21/11/2022

A MALAWI MUSADANDAULE ZA NVULA CHIFUKWA ANDUNA A ZA ULIMI APITA KOIGULA KU IRAQ

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Lilongwe