Miracle Technical College
19/05/2026
Pali ndalama apa. Tiyeni nazo!
Private Technical Colleges Association of Malawi-PRITECAM
Koda Ida.
Osanamizira kuti sitinawerenge uthenga uli mmusiwu. Tiyeni tikawone zotsatira za mayeso!
Results for December Summative examinations are in. Students can check with their Heads of Sections
14/05/2026
Si tsiku lililonse timalowa n'class guys, limafika la Kamuzu timapuma.
12/05/2026
Amisili tonse tabwerani pano.
Boma latsekula khomo kwa mmisili wina aliyense kuti akalembetse nkukhala ndi kalata zogwilira ntchito yake mdziko muno. Khomoli alitsekula kwa mmisili yemwenso sanalowe mkalasi Kuti akaphunzire za luso. Kuti mutsate zambiri werengani kalata zili mmusizi komanso m***a kupita ku ofesi zaboma zoyeza luso la manja ku Mzuzu, Blantyre komanso ku Lilongwe ngakhale ku likulu la unduna owona za ntchito.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the university
Telephone
Website
Address
Karonga Airport
Karonga
Opening Hours
| Monday | 08:00 - 16:00 |
| Tuesday | 08:00 - 16:00 |
| Wednesday | 08:00 - 16:00 |
| Thursday | 08:00 - 16:00 |
| Friday | 08:00 - 16:00 |
| Saturday | 07:00 - 18:00 |
| Sunday | 08:00 - 12:00 |