LIL JAY MW

LIL JAY MW

Share

21/05/2026

Osazakhulupilira ma ubwenzi popeza yemwe ukumukonda lero ndi ex wa wina wake ndipo analonjedzana Kuti sadzasiyana pano anasiyana koma ankati i can't live without you pano akukondana ndi munthu wina ndipo Ali Moyo bwinobwino.

Zachikondizi pena pake sungazimvetsese

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Karonga?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Karonga