Mwano

Mwano

Share

21/07/2025

Pepa maliya ndilore chibwezi tidzalemera kukhala ndi ana 5 okha pa 16 September

06/03/2024

Kod asisi kubanjako mupita ndi sim card lomweli

24/02/2024

Kodi mchifukwa chiyani munthu akafa amanva kuyabwa kuphanzi

Ankolo akufusatu uku

24/02/2024

Kill me โš”๏ธ 990 million Cash
Marry me ๐Ÿ’ 50 million Cash
Date me ๐Ÿ’ 5 million Cash
Kiss me ๐Ÿ˜˜ 3 million Cash
Ndidziwe adani lero๐Ÿ™Œ

23/02/2024

Umphawi ukati ukukakamire๐Ÿ™Œ

Ogulitsa ma apples ๐ŸŽ pa Kanengo anatola ndalama zoposela 1.5 Million zomwe nkulu wina akuti zamupulumuka, iyeyokuzitenga okhulupilika kukauza a chairman oyitanila ma minibus, chairman uja anamuuza mwana kuti lowa mu chimanga tikagawane, chigulu chaona ndalama kuyamba kuzilimbilana ndalama kumangong'ambika.

Pomwe anthu amabalarika mwana uja wapezeka ndi ndalama zokwana K4000. 2K yong'ambika ina ya bwino-bwino, ma apples alibe Malaya ang'ambika, a Chairman aja alibe kalikonse ngakhale phone alibe ena atenga๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿ™Œ

23/02/2024

Ndikudekha mu mponela inu mulikuti

23/02/2024

Musadagone ikani mau awa muchingerezi"onetsa umuna wako mphwanga๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜๐Ÿ˜

Follow mi for more updates

23/02/2024

Saint ndi dolo "Ndan" wapha

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Domasi?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Brantyre
Domasi