RedArc Media Blog

RedArc Media Blog

Share

03/05/2026

Awa nde akazi Osamala banja,😂 Cheating Samapanga nawo

Photos from RedArc Media Blog's post 03/05/2026

JOMO SANALAKWISE KUMU PHETEMULA MAI UJA OKUBA AJAIRA KWAMBILI MU LIMBE-watero MALONDERA

Mkulu wa achinyamata mchipani cha MCP Hon Steve Baba Malondera MP wadzuzula mfumu ya mzinda wa Blantyre Isaac Jomo Osman popepetsa pa zomwe anachita zomwe wati mfumuyi siyinalakwitse.

Malondera wati ngati mtsogoleri umayenera kuyima pa chiganizo chomwe udachita. Iwo apereka chisanzo cha malemu Dr Bingu Wa Mutharika kuti analankhurapo kuti wakuba aomberedwe ndikuphedwa komanso anayikira kumbuyo IG Peter Mukhitho kuti sakupepesa kwa aliyense.

Malondera wati munthu wakuba safunika kumsekelera koma kuthana naye chifukwa ndi munthu opanda chisoni. Phunguyu wati iye ndi mmodzi mwa anthu omwe anachitiridwapo chipongwe ali mnyamata mu Limbe mpaka kupanidwa ziwalo za abambo.

Phunguyu wati onse omwe akudzuzula Jomo akuyenera kuzaberedwapo kaye, kapena mwana wake, mkadzi wake mwianaso Mayi ake azigwiliridwe ndi anyamata achifwambawa ndipomwe azaziwe kuwawa ndipo azaziwa njira yothanirana ndi akuba.

Want your business to be the top-listed Media Company in Chichiri?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address


Lilongwe , Zomba, Mangochi And Mzuzu
Chichiri