ICBM DAWAH CLUB

ICBM DAWAH CLUB

Share

07/04/2024

Zakatul fitr iperekedwe before swalah ya Eid ndipo tipereke chakudya chodyedwa ku dela lomwe tikupelekalo... chakudya not ndalama ngat muli nd ndalama zambiri kagulen chakudyacho(chimanga or mpunga) nachipereka

28/03/2023

الحديث اليوم
قال رسول الله صلى الله عليه وسلم : (من نسي وهو صائم فأكل أو شرب، فليتم صومه فإنما أطعمه الله وسقاه)
رواه مسلم

Mtumik wa Allah S. A. W adat:
Kwamene wasala ndkudya komanso kumwa moiwala, akuyenera apitilize swaum yake ndithu ndi Allah amene wamudyesa iye ndkumumwesa.

Mu hadith imenei ak*t kuiwala. Kuiwala kulibe mankhwala komanso kuiwala samachita kukonza
Allah alandire kusala kwathu

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Blantyre