Pakachere Institute for Health and Development Communication

Pakachere Institute for Health and Development Communication

Share

20/11/2024

Zathu Pa Wayilesi.... Lero iyamba 2 koloko pa MBC 2...

Program ya lero iyamba 2 kokolo pa MBC Radio 2. Tisaiwale pali kusintha kwa lero lokha. Komanso paja kuli chimpikisano cha 'Comment to Win'. Omwe aiphula pakali pano sabata ino ndi Pek-One Fih Sure komanso Dan Thanganyika ndipo awina ZATHU branded bottles. Tiyeni tipitilize kupanga share post ina iliyonse yomwe ituluke sabata ina iliyonse kutsogoloku. Pangani share, khalani ndi ma comment komanso ma likes ambiri. Mukatero muwina kaya Umbrella, T-Shirt ndi zina zambiri. Mvetserani lero program ya ZATHU pa MBC Radio 2. 2 koloko ino.

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address


P. O. Box 30248
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00