A Inno Busy
06/07/2026
Ndakhala ndikuona kuti ndakhala zii osakupasani nyimbo zambiri posachedwapa. Pali zinthu zosiyanasiyana zomwe zinandipangitsa choncho. Zina ndinazigonjetsa kale, zina ndikulimbana nazo pano.
Chifukwa cha zimenezo sindimakhalanso m'ma show komanso sindimatulutsa nyimbo mwa apo ndi apo.
Koma lero ndati ndikuuzeni kuti ndabweranso ndi moto! Cholinga changa ndi chimodzi: kukusangalatsani inu nonse okonda nyimbo zanga
05/07/2026
Cha Dropa!🔥🇲🇼 New from MED C MW 👇
https://youtu.be/3E6ycWmvM4U
04/07/2026
Am listening to My upcoming Ep koma eeeh 🔥❤️🔥🙌🙌 100% ready to give my fans GOOD music …… (comment box )
04/07/2026
Jully 🔥
ZOMBA
BLANTYRE
Pressure Live on stage 🔥
https://youtu.be/F0jW2ekU-5g
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Blantyre