Finaltouch
06/06/2026
Khasu silimakhala lokongola inu, umakhala okongola ndi mpeni odulira cake et? kkkkk apapatu ndipomwe pamachitikira matsenga athu , ka battery akaka kamapanga zamatama customer anakagula ndikungosiya kwa 2moths osakagwiritsa ntchito ndiye kanaloka.
Eya battery limakhala ndi firmware ndipo firmware imeneyi imapanga detect changes in voltages and current mukamachaja or mukamagwirita ntchito, Ngati mwangosiya battery lanu osatchaja kwa nthawi yayitali voltage imatsika mpaka below the optimal voltage, zikatere firmware ija imaloka kuti ma cells asafoile.
So ngati izi zinakuchitikirani dziwani kuti battery la PC yanu ndilotheka kukhala ndi moyo.
NOTE : Ma battery ena amakanika kukhoza chifukwa IC kapena firmware yake siili supported ndi Battery Analyser.
Nthawi zina zimafunika nthawi yaitali kuti battery lipangidwe calibrate siza 30 minutes yatheka.
05/06/2026
Zomafunsana kuti aise sand paper bwanji tipangire clean chootchelera kapena kumazitama kuti muli ndi ma jeans abho mumangokhukhuza soldering iron pa trouser nzachikale ndipo ngati mukupangabe muzazindikira kuti mumachedwa mukadzangoyesa ka Soldering Iron Tip Cleaner akaka.
Ubwino wake momveka bwino ndi uwu;
Soldering iron tip imakhala ya clean heavy,
Soldering iron tip imakhala yolimba chifukwa temperature simapidwa affect popanga clean.
Soldering iron siimachepa size
iiii basi ndatopa ndikulemba kwinako muzipanga comment nokha mukagula.
04/06/2026
Or muwafunse anzanuwo ifetu tilibe nsanje, Timakonda kuti aliyese azikhala osangalala makamaka masomphenya ake okhala Technician wa bho akwaniritsidwe thats why sitimabisa info.
Inuyo ngati mulibe BIOS Programmer koma mumakonza ma PC nthawi ija ndi ino kuti mupeze yanu pa price ya bho pati.
Inuyo kugula akaka simunabetse coz simungaflashe ma computer 5 yake isanabweze. Izizi ndikunena coz i love you.
04/06/2026
Zomagogoda waya kapena kumasulira mpeni ma device anu si deal.
Tayesaniko ti ma set ta sharp iti.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Livingstone Avenue Limbe
Blantyre
312229
Opening Hours
| Monday | 08:30 - 17:00 |
| Tuesday | 08:30 - 17:00 |
| Wednesday | 08:30 - 17:00 |
| Thursday | 08:30 - 17:00 |
| Friday | 08:00 - 17:00 |
| Saturday | 09:00 - 14:00 |