PKM Design

PKM Design

Share

25/02/2026

With Agora Limited – I'm on a streak! I've been a top fan for 5 months in a row. 🎉

22/09/2025

Aliyense njila yake ndiyosiyana ndi wina

Mayi awa ndi Graça Machel. Mayi yekhayo yemwe anakhala first lady wa mayiko awiri osiyana.

Anali mkazi wa Samora Machel ku Mozambique (1975–1986).

Kenako anakwatiwa ndi Nelson Mandela ku South Africa (1998–2013).

Ndi mayi olimbikira payekha.

Anavekedwa title ya Dame Commander of the Order of the British Empire mu 1977, ndi Queen Elizabeth ll chifukwa cha ntchito yake ya women and children's rights.

Sidenote
You are whatever you believe yourself to be

25/08/2023

BREAKING NEWS


MWANA WA MASIKINI WAPHEDWA

M'mawa wa lero ana amasikini atatu anavulaza ndikulanda bambo wina katundu wake pomwe amadutsa nsewu mudi via makhetha.

Bambowa alandidwa ndalama, nsapato komanso avulazidwa pobayidwa ndi mpeni nkhope.

Polimbana ndi anawa, iwo adakwanitsa kugwila mwana mmodzi ndipo anakuwa kupempha thandizo mpomwe khamu la anthu lidatulukila.

Anthu achifundo adakwanitsa kuwatengela bambowa ku chipatala ndipo ena anayamba kumenya mwanayo mpaka kupha.

Want your business to be the top-listed Advertising & Marketing Company in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Blantyre