Prophet Y Simujah

Prophet Y Simujah

Share

25/12/2025

NDI ANTHU OCHEPA KWAMBIRI OMWE AMAYAMBA CHI KRISTU NDIKUCHIMALIZA MOYENERA.

➖Ngati munthu sakukwanisa kumvera bwino-bwino Mulungu,amagwa,apo ayi amalowedwa mizimu ya chisocheretso.
➖Timayenera tikhale anthu omvera kwambiri ngakhale mu zithu zomwe sizikutipasa tanthauzo.🙌

28/05/2025

KHALIDWE NDILOFUNIKA KWAMBIRI

🌹Ena adati Khalidwe ndi chuma,mau amenewa ndi anzeru kwambiri chifukwa ndaona anthu ambiri akulephera kupeza znthu zabwno kamba kosowa Khalidwe.
🌹Asikana ambiri akulephera kupeza ma banja abwno chifukwa chosowa Khalidwe,ena mwano,ena Kuzikuza,ena chipongwe ndipo ena chifukwa Cha moyo wawo wa social.🙌

29/03/2025

KULIKHIDWA KWA MTENGO WAUTALI KU MALAWI 🇲🇼💔

➖Zithu Zina zooneka ngati zosakoma zikamachitika ku Dziko anthu ambiri amangoganiza kuti akuchita ndi satan.
➖Ayi ndithu,Zina zimakhala kuti akuchita ndi Mulungu kuti anthu amphunzilepo kathu {Alape}.
➖Mtengowu mu Dziko lauzimu ndimaona kuti akuulikha ndi Mulungu mwini osati Satan,ndpo Mtengowu wakhala ukupasidwa ma WARNING ochuluka koma udaumisa khosi kamba ka mapangano adziko lapansi omwe udalowa.
⚠️Mtengowu ukalikhidwa anthu ambiri ku Dziko azayakhula zosiyana-siyana zonyoza anthu ena koma omwe mungawelenge post yi musazayakhule nawo chifukwa akupanga izi ndi Mulungu mwini.

Want your place of worship to be the top-listed Place Of Worship in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Machinjiri Khama
Blantyre