Help me

Help me

Share

01/10/2024

Pano mitu siikugwira ayi. Akuyesela kuupukusa km opanda nyanga. Nkhani ndi mwana wa miyezi itatu. Akulira mosaneneka akayamba kulira akumakana chilichonse. Andifunsa ine chothandizo Cha momwe angamuthandizire mwanayo ndangowauza kt apite kuchipatala km akt apita koma sakupeza Vuto. Kupita kwa asing'anga sakupeza Vuto kumapemphero akumati akabwerako zikumayambikanso ndiye athandizeni a neighbor anga. Anzango omwe mukudziwa zochita please help me

08/10/2022

Uyu ndi *Sebastian Joseph* mnyamata wa zaka 13, yemwe wasankhidwila secondary ya boma ya Likuni Boys kuchokela pa Namachete Primary(Zomba). Kwawo ndi kovutikisisa amakhala ndi mai ake okha omwenso amadalila ulimi wokha. Tikupempha chithandizo kwa okufuna kwabwino k*t athandize chifukwa sangathe kulipila school. Aphunzitsi ake ayeselako kusonkha transport ndi kandalama koyambila koma nzosakwanila. Omwe angafune k*thandizapo atha kuimba pa 0992876139(mai ake) kapena 0884151637(deputy)

Want your business to be the top-listed Grocery Store in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Website

Address


Nyambadwe
Blantyre