Health tips

Health tips

Share

27/01/2026

Zizindikiro za mauka ni monga:
- *Kumva kuyabwa ku maliseche*
- *Kufiira kwa kumaliseche*
- *Kutuluka madzi kapena chikazi chochuluka komanso cha fungo*
- *Kumva kutentha komanso kupweteka kumaliseche*
- *Kumva ululu mkazi akangomaliza kugonana ndi mamuna olo kapena ululu akangomaliza kukodza*
- *Kutuluka tinsungu olo zilonda kumaliseche a mwamuna*

Zomwe zimayambisa mauka ni:
- *Bacteria or fungi*
- *Nyongolosi za mumatumbo*
- *Kuchepa kwa vitamin b nthupi*
- *Mankhwala (chemicals)*
- *Zopaka paka ndi kupopera mu pheche mpeche olo nthupi*
- *Kuvala zovala zothina kwambiri monga ma panti*
- *Kuvala zinthu zokuda komanso zonyowa monga mapanti*
- *Umve wa mkati*
- *Nthenda ya shuga komanso ma antibiotics*
- *Kusavala ma panti monga kwa inu adzimayi idzi zimapangisa kuti fumbi lidzilowa ku ndata kwanu*
- *Mankhwala ena*
- *Adzimai ena amatha kukhala ndi mauka chifukwa choti ngoyembekedzera*
- *Zakudya zomwe zili ndi shuga kwambiri*
- *Zokumwa zoledzeretsa*
- *Kugonana mosadzitetedza*

Ipa pali zipangizo zomwe zingakuthandizeni kupewa mauka:
๐ŸŽฏ Mukamaliza kugonana musavaleso pant๐Ÿ‘™ unless maliseche muwonetsetse kuti awuma and mwatsuka.
๐ŸŽฏ Musamakonde kuvala zonyowa.
๐ŸŽฏ Musamavale pant๐Ÿ‘™ mmodzi modzi.
๐ŸŽฏ Nthawi zina ma pant anu muzichapako ndimadzi otentha or muziyanika padzuwa osamangoyanika pamthuzi.
๐ŸŽฏ Ngati mulindivuto losachedwa kutuluka madzi kundata ngati mukuyenda muzivalira nyanda pant wanu๐Ÿ‘™.
๐ŸŽฏ Mukamaliza kukodza muziwonetsetsa mwadzipuputa mikodzo yotsalirayo phuzilani kuyenda ndi tissue mu hand bag๐Ÿ‘œyanu osamangodziwa kusungila face powder ๐ŸŒ.
๐ŸŽฏ Mukamapita kosamba muzichapilatu pant ndikukayanika then kuvala wina osamasungila kuti mudzachape akada mapanti ambiri.

Mukusowa mtendere ndi mauka, bwerani ku inbox ya _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ tili ndi mankhwala othetseratu matenda amenewa ndikuyambaso kukhara moyo wantendere osati omangodandaula ayi. Tipezeni kuno ku _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ ngati muli kutali timatumiza ndipo mankhwala adzakupezani mosavuta 0885777241/0997088677.

Kuna ndani amene ali ndi swali kapena amafuna kuziwa zambiri pa mauka?

Photos from Health tips's post 14/07/2025

ZOOMAX PLUS

azimayi uyu zoomax plus makhwala mbambande obweletsera matako ndi ma hip.
Makhwala opangidwa kuzipatso ndikuzitsamba omwe alibe chiospyezo chinachilichonse ku thupi lanu.

Matsiku anowo azimayi ndikuuzeni chinsinsi Cha azibambo, deal ndi chikhaliro ati khope azaona pamaliro. Nde chikhalirocho kuti chigwire bwino chinjanjepo bwino akaka ka zoomax plus.
Makhwala
1. Amabwelesa ma hip
2. Amabwelesa matako
3. Amanenepesa zonse thupi, kuti thupi lija lizifanana ndi thako labwera lija. Osati thako lino koma ka thupiko nde kang'onong'ono.
4. Zoomax amasalalisa khungu ukamwa zoomax sikuti nkhani ndi nyashi yokhayo ayi mumasalala. Amachitatu kumukongoletsa mkazi, kukongola ngati umasambira mkaka
5. Kwa omwe ali makandamtchembere/ma stretch marks ukamwa awa zimachokaso, osati nyashi yabwela makandamtchembere mbweee ayi.

Tili naye pa mtengo omvelera mthumba ndipo tikupezekela ku msika wa Ndirande and Magalasi kutali timatumiza pa courier ndi ma bus...
Contacts: 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 02/05/2025

FAT BURNER

kuli anthu Ena omwe ndi onenepa koma kunenepa mopitilira, anapitiliza mulingo.ananenepesa. Inu kunenepatu nkwabwino koma kuliso ndi ma health issues ake kotero nenepani koma size yabwino. Nde kuliso Ena Ali ndi zimmimba. Basi mmimba khutchakhutcha aaaaa guys be serious.

Koma tili ndi fat burner uyu, amamphwesa thupi komaso kuphwesa mimba.
Ma girls kuphwesa mimba mukatchena kumaoneka ngati wa mmagazine.
Sizokhazo amalipanga refresh thupi makhwala awawa .
Komaso ndi body cleanser amachapa mthupi.
Inu muchedwelanji.
Tipezeni ife tili ku msika wa Ndirande ku Blantyre komaso kwa Magalasi 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 17/04/2025

TALATIN 30

China mwa chomwe chimafotokoza kuti uyu ndi mkazi ndi hip. Atleast azimayi kumakhalako ndi hip .
Mkazi akaima kungoti see ngati paima pholo lamagetsi. Nde bolaso phaulo limakhala lamabumbump.

Ndiye product yomwe imabwelesa hip ina mwa Iwo ndi Talatin 30.
Uyuyu ndi matablet ndipo mkazi akamwa amachita kuumbika bwino Ka hip Ka bwino kaja kogwilika.
Nalo thupi limachita kutakasuka. Thako lizinjanja osati thako kungoti mphwathalala.

Nde talatin 30 tili naye ife pa mtengo omvelera.
Tili ku Blantyre Kwa magalasi ndipo anthu omwe muli kutali timatumiza.
Contacts: 0885777241/0987474035

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Nyamambadewe
Blantyre