All connection connecter Agent
UBWINO WAMASAMBA ACHAM'MWAMBA KAPENA KUTI MORINGA🌳
```Musabalalike ndimau oti Moringa dzina lanchichewa ndi CHAMMWAMBA ngati simukwadziwa masambawo afunseni anzanu sizimasowa izi```
*1.KUNENEPETSA THUPI.*
✍️Kuyanika masamba aawisi a moringa mum'thudzi ndi kusinja akawuma ndi kusefa. Ufa wakewo umanenepetsa ukamathira m'phala. Ana onyentchera ayenera kumalandira moringa m'phala kuti anenepe.
*2. KUCHOSA MATENDA OSIYANA SIYANA NTHUPI.*
✍️Mukamadya pothira m'phala ufa wake, mudzapewa kutentha thupi, chifukwa cha m'mapapo, matenda a maso ndi m'khutu ndipo yemwe akudwala matenda a HIV/ Aids zimakhala bwino kumadya Moringa chifukwa matenda osiyanasiyana amachepa.
*3. KUWAWA KWA MUTU.*
✍️Kutikita pa chipumi masambawo kumathandiza kuziziritsa mutu komanso potafuna nthangala zitatu za Mulinga kumathandizira kuti mutu uleke kuwawa, matenda a shuga amachepa, zilonda zam'mimba zimatha ndipo chiseyeye chimatha mu usinini.
*4. CHILONDA CHOCHEKEKA*
✍️Ngati mwachekeka sinjani masamba anthete a moringa ndi kumata pochekekapo ndipo matenda ena salowapo komanso sipamatupa.
*5. MATENDA A LINYESU.*
✍️Ngati mwadwala matenda alinyetsu, matani zosinjidwa zija pamalopo.
*6. ZILONDA ZAMMIMBA.*
✍️Tiyi wa masamba a moringa amathandiza kuchotsa zilonda zam'mimba komanso kuthetsa kutsekula kwa m'mimba.
*7. KUSOWA KWA MAGAZI NTHUPI.*
✍️Mu moringa muli 'Iron' wambiri yemwe amathandizira kupanga magazi. Ndiye pachifukwa ichi, odwala onse osowa magazi, amawalimbikitsa kumadya moringa posakaniza zakudya zawo.
*8. KUBWELESA NKAKA MMAWELE*
✍️Amayi oyamwitsa azimwa chakumwa chopangidwa ndi maluwa a moringa powiritsa maluwawo. Mphamvu ya maluwa a moringa imathandizira kupanga mkaka wambiri mwa mayiyo.
*9-KUTETEDZA CHIKHOZODZO*
✍️Chakumwa chomwecho cha maluwa a moringa chimathandiza kuti njira zotulutsira mkodzo zisamakhale ndi matenda.
*10 -KUCHOSA NYONGOLOSI ZAMMIMBA.*
✍️Mukamadya zibalobalo za moringa za nthete,mudzachotsa nyongolotsi
0993500406 sms
Mwaswera bwanji masana ano?
*KUTETEZA NDI DIMA MBEWU ZANU OR PAKHOMO KWA AKUBA*
🌳🌳🌳🌳🌳🌳🌳🌳🌳
🌳pena akuba amadzuza kwambili koma apaseni chidima akafika pa nyumba or kumunda akafuna kuba zinthu azingodusa ndikupita kwa anthu wena .
Pangani izi👇
>Fupa la nkhumba lakare
>Sontho
>Mpoloni
>Manyi akare
>Mwavi
🌳mangani pa nsalu yantundu wakuda ndipo lavulilanimo malovo ndikunenelela mau awa👇
👉Ngat alipo amakonda pomwe Pali manyi or kubwerelapo nde kuti akubaso azaonapo zabwino pano Koma ngat aliyese amapanga mselu ndi manyi akuba naonso azinyanyala ndikudusa pakhomo /pamunda pano asaonemo chanzelu .
🌳kumbilani pakati pa Munda or pakhomo ndipo palibe azakuberani ,
🌳paja kupewa kumaposa kuchiza pangani izi ndizophweka koma zimathandiza kwambili.
Sms 0993500406
Mwaswera bwanji konse komwe muli?
*ZINTHU ZOCHITISA MANYAZI KOMASO ZOKUONESANI CHISILU PAMOYO WANU* 👇
1⃣ Ngati sukubereka
2⃣ Mamuna wachida chonga ka 🥄 teaspoon.
🐢 1⃣, mundimvesese bwino bwino ,utha kukhara ndi chilichonse koma ngat ulibe mwana umatengedwa chizete and anthu amakunyoza muli mose momwe angalankhulile ( *umva mwamuona mkaziyu eti akungozazisa chimbuzi tere alibeko mwana chibwerereni pamudzi pano* ) nde zimakhala zinthu zowawa koma ife opanga makhwara achikudawa tikati makhwara ndi awa mumati ai ineyo singapange zachikuda mmmm pepani siku lizakwana muzawafuna achikudawa azakuthandizani.
Pangani izi ngat anakulozani ena ake kuti musakhare ndi mwana👇
>Pezani palibe kanthu
>Kasuluzya
>Midzu ya mposa
>Midzu ya CHISOSO chogonera
>Midzu ya kabatika
🐢kuwilisa kumamwa mamawa ndi madzulo kwa 14days, kaya ndiwe mamuna or nkazi uli ndi vutoli koma lochita kulozedwa muzabereka bwino bwino Inu si mungakwanise kupanga ,okozedwa kare ulipo koma ndi k35,000.
🐢 2⃣, Nde paliso azibambo wena oti chidachi chimakhara ngat chinachita kulumala koma ai ndi mene anabadwila ,tunena kachida kakafupi ,komaso Kali kakang'ono moti akazi amachita kuthawa ( *amvekere eeee mamuna uja amangondiseweresa ndi kanchila kake nde sindikumvapo kanthu ai kachida ngat kachara ka mwana mmmmmmm)*
🐢Inu osavutika makhwara awa apa 👇
>Chipaso Cha mvunguti
>Sabola wantchire
>Kapantha
>Mwavi
>Nthutumuska
🐢basi inuyo mukhara ndi chida chabambo sopano not kachida ai akazio azakuthawani chifukwa cha ka spoon kanuko ,mamuna azioneka pogwila ntchito ndipo munthu wamayi azichita kuyamika kuti yes inuyo muli ndi chimudaliso koma inuyo palibepo ndi tsiku limodzi pomwe anakuyamikaniko mmmmm
Sms 0993500406
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre