True keyz

True keyz

Share

25/03/2023

Bhooom oyimba waku machinjiri nkuzandiyimisa kt andi pemphe ndimbe🀣🀣🀣mxieeeewπŸ™„
Me:kagulileni dollar yomwe ndina lipilila pa door ku show yanu😎✊πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Photos from True keyz's post 08/01/2023
29/08/2022

True fans wat do you think πŸ€”
Supporting this will mean so much love ❀️ you hv for others πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ™πŸ™. Plz do something to help them

From the Inbox

Chonde ndithandizeni ndasowa mtengo wogwila. Ali pa chithunzi yo ndi sister wanga, Magret Phiri. Anabadwa 1990 ndipo ali ndi ana 4.

M'modzi anasiya kuyamwa kamba kodwala kwa amayi ake Maggie wakhala akundwala kwa nthawi yayitali koma vuto ndi mpweya omwe usowekela kuzipangila okha ndipo wankhala ali mchipatala kwa miyezi 8 kuchokela January mpaka pano ndipo adoctor anawauza kuti ngati patapezeka Oxygen komanso magetsi odalilika atulusidwa ndicholinga choti akapitindwe mphepo ina panja pachipatala.

Mwayi opeza oxygen unatheka koma chifukwa chakuzima zima kwamagetsi sizingatheke kuti apite kunyumba.

Pempho lathu ndi generator kapena solar kuti tizigwiritsa ntchito kunyumba chonde muchipatala tatopa kukhalamo.

Amene angatithandize ndi njila Ina iliyonse yopezela magetsi odalilika, nambala yanga ndi iyi +265 881 62 02 58 komanso atha kubwela ku chipatala kuno azachitile umboni.

Chonde ndifikitseni uthengawu kwa aMalawi chonde

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Shoprite Highway
Blantyre