OSAKA Nasheed PRO
24/11/2025
Bwalo lalikulu loweruza milandu mawa pa 25 November 2025 likuyembekezeka kumva ngati kuli nkoyenera kupereka chiletso choletsa mzikiti wa Kachanga ku chileka m'boma la Blantyre kupanga adhan.
Sukulu ya Kalibu academy ndi yomwe inapempha chiletsocho ponena k*ti kuyitanira anthu ku mapempheroko kukumadzetsa mphokoso lomwe likumasokoneza ntchito ya maphunziro pa sukulupo.
Oweruza milandu Justice Tembo ndi yemwe amvelere mlanduwu.
assalaam alykm warhamatullah wabarakatuh
followers
13/09/2025
#1. Nde chi abayacho chiguduli tu munthu kubvala abaya ngat wabisala mu carpet🙄🙄🙄
#2. muslim girls lets be honest
Titat takupatsan 1650 pa sula iliyose munaloweza nde k*t muonjezera zingat k*t mukagule abaya?
#3. Abaya ngati raincoat 🤣🤣🤣🤣🤣Chi umbrella tu ati atamangira lamba wake phaaa! Ndendende!! Mtolo wa mzimbe ine ndimafuna tu kukhala Chete koma ayi pepani🤣🤣🤣🤣🤣inu muzibvala ma dress aja mumakongola
#4. Ndavomeleza
Abaya ndigula
Koma everyday pogona
Uziwerenga Quran
First page up to the last one.
#5. Munthu umatopa ndikusoka ma abaya
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Website
Address
Blantyre