5 MOBA
30/03/2026
MAFUTA AKUPEDZEKA CHIFUKWA AKUDULA_Simplex Chithyola
Nduna ya kale ya za chuma a Simplex Chithyola Banda ati mafuta a galimoto akupezeka m'dziko muno chifukwa chak*ti anthu ambiri sakukwanitsa kugula pa mtengo wa pafupifupi 5 sauzande kwacha pa litre.
Iwo ayankhula izi pocheza ndi kanema wa Zodiak.
A Chithyola Banda atinso ena mwa mafuta omwe akufika m'dziko muno ndi omwe boma la MCP lidaitanitsa mu nthawi yawo.
Iwo ati ndi okondwa k*ti pakadali pano boma la DPP lik*tsatira ngodya zinayi zomwe iwo adakhazikitsa zokhudza chakudya, fetereza, mafuta a galimoto ndi ndalama za kunja.
Anthu omwe amayankhulapo pa zinthu zochitika m'dziko ati ulamuliro wa MCP sukuyenera kumadzitamandira pa nkhani ya mafuta a galimoto potengera ndi mavuto omwe aMalawi amakumana nawo pa nkhaniyi mu nthawi yawo.
Wolemba Vincent Chigalu Onyauda, Chinthebe Thyolo
14/02/2026
Big shout out to my newest top fans! 💎 Maulana Mdala Banda, Blessing Lufan, Charles Matias, Joseph Chriford, Henery Christopher, Mohammed Silencer, Traube Chisalex, Osman Jafali, Bertha Wa Isaac, Finias Mkango, Rainford Phalira, Eric Chilumpha, Zephaniah Kawanga, Rabson Coster, Kondwani Musachi, Owen Kambenje, David Kamgoga, Aimen Chimbalanga, John Jamali, Bambo Storey Nkhanie, Palley Kananji, Jailos Soko, Andrew Majamanda, Prince J K Mphatso, Mozwell Kathumba
Drop a comment to welcome them to our community,
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Website
Address
Uitenhage
6241