GoalLine Media

GoalLine Media

Share

05/02/2026

Team ya Masters Security inayimitsa kaye zokambirana ndi Khuda Myaba kuti athane kaye ndi team yake yakale ya Scotland.

02/02/2026

Bob Mpinganjira wati kugonga ndi anyamata a Mzuzu City Hammers amene analimo ochepa zaonetserathu kuti anyamata ake sanasewere mpira omwr iye amayembekezera.

02/02/2026

Tikukumana ndi team ina koma ife ndi Khumbo lathu kuti titenge chikhochi watero m'phunzitsi ongogwirizira wa Mzuzu City Hammers Lazarus Deco Nyemera.

29/01/2026

FCB Nyasa Big Bullets alengeza kuti aphunzitsi 16 ayika ma application pa udindo wa head coach womwe uli vacant, pomwe 14 ndi achilendo ndipo awiri ndi aphunzitsi am’dziko muno.

Telephone

Website