Mr Chicken
11/02/2026
Nkhuku zazikulu bwino komanso zokoma zikupezeka ndi Mr Chicken, Kwa Mponda bwino market pa mbewa,Zomba.
Mukhozanso kutiimbira phone pa manambala awa:
0999662483/0888 715 444
Mr Chicken - Growing quality, Haversting Trust.
https://www.facebook.com/share/1JwX4KrHVQ/
09/02/2026
THE BEST CHICKEN SUPPLIERS IN ZOMBA
We sell Live and Dressed chikens, In small and large quantities. Chicken parts also available
Location: Mponda bwino market pa mbewa.
Hotline: 0999662483 / 0888 715 444
07/02/2026
Budget ya ndiwo isakuphwanyiseni mutu akasi !!!
Nkhuku zathu ndi Mk19,000 (Zamoyo), Zokupha kale ndi Mk20,000 yokha basi. Tabwerani kwa mponda bwino pa mbewa muzagule.
Mr Chicken - Growing quality, Harvesting Trust.
30/01/2026
Kodi muli ndi ukwati, chinkhoswe, party, nsonkhano kapena maliro ndipo mukusowa amene angakupangeni supply nkhuku zambiri pakamodzi ?
Ife a Mr Chicken tili pano kukuthandizani mwamachawi komanso moyenera.
Kaya mukufuna nkhuku za moyo kapena zokupha kale ifetu imeneyo sinkhani komanso pa mtengo wabwino
Tiyimbireni lero pa: 0999662483 / 0888715444
Komanso timapezeka kwa Mpondabwino market pa mbewa, Zomba.
28/01/2026
WE SELL LIVE CHICKENS, DRESSED CHICKENS, AND CHICKEN PARTS AT AN AFFORDABLE PRICE
LOCATION: Mponda bwino market pa mbewa,Zomba.
HOT LINE : 0999662483/0888715444
Mr Chicken - Growing quality, Haversting Trust.
https://www.facebook.com/share/1JwX4KrHVQ/
Mr Chicken Mr Chicken is a trusted poultry company offering live broilers, dressed chickens, and quality chicken portions at affordable prices. We supply both small and large quantities and cater for all types of events. Growing Quality, Harvesting Trust
28/01/2026
Nkhuku zazikulu bwino komanso zokoma zikupezeka ndi Mr Chicken, Kwa Mponda bwino market pa mbewa,Zomba.
Mukhozanso kutiimbira phone pa manambala awa:
0999662483/0888 715 444
Mr Chicken - Growing quality, Haversting Trust.
https://www.facebook.com/share/1JwX4KrHVQ/
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Zomba