Willy Mbewe
Mudazindikira liti kuti nyerere ndi mankhwala a nsikidzi?
Lero ku Limbe andilanda jumbo๐ณ๐ณ
Team ya Liverpool yamwalamwazika๐ ๐ ๐ ๐
Sanandiuze kuti chantha ndi nagoona DP ayikapo wina๐๐๐๐๐
Moni
Ine kumudzi ndi ku Lilongwe ndi ku Thyolo
Inu kwanu ndi kuti?
06/12/2025
Mzibambo mukumuona pachithunziyu Analuza moyo wake after atapangidwa surgery kumalo ake obisika kumene kunatupa chinthu monga mukuonera pachithunzipa.
DON'T PASS WITHOUT SORRY ๐ฅ๐ฅ
Lero mwadzuka bwanji abale nd alongo
Koma kuyankhula ukuku pali chimene chichitike kuthandiza a Malawi?
Queen Sheba kulimba mtima kumeneku akukutenga kuti?
Kodi nkhani ya oyimba wathuyi ndiyowona?
Koma Chakwera adatilera mopusa ku nkhani yamagetsi yokhayi. Apa magets akungokhala ngati oyendera mphepo ndithu๐๐
11/09/2025
Akaka wina akamvera mfungo next week๐ ๐
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Zomba