Chapter Beat's
11/10/2025
DPP YAYAMBA KUMANGA MA UBALE OMWE CHIPANI CHA MCP CHINAPHWATSULA PAKATI PA DZIKO LINO NDIMAYIKO ENA MONGA CHINA NDI USA
Chipani cha, Democratic Progressive Party DPP chayambapo ntchito yomanga ma ubale omwe chipani cha, Malawi Congress Party MCP chinaphwatsula pakati pa dziko lino ndimayiko ena monga, China ndi USA.
MCP inaphwatsula ma ubale apakati pa dziko lino ndimayiko ena monga, USA, China kuzela munjira zoyipa monga katangale, kuba komanso kuzembetsa zigawenga zoopsa ndizinthu zina.
Kutha kwa ma ubale pakati dziko lino ndimayiko ena kwakhala kukusoneza kwambili ntchito zaboma komaso kukolezela mavuto pakati pa anthu mudziko lino.
Pofuna kuwonesesa kuti zinthu zabwelela muhimake nduna yoona nkhani zachuma, Joseph Mwanamveka anakumana ndi kazembe wadziko la China ndikukambilana zamomwe dzikolo lingathandizile dziko lino.
Pangan Follow page iyiππFigoh Mw kt zisakudusen
08/10/2025
Ambuye ndiwabwino ikakhala ntchito ndye ndikugwila km ikuchedwa nd nthawi kt ikwane. Ndye pot mawu amat OSATOPA Osafooka OSAOPA zabwino zili msogolo nafe nthawi ixakwana tizapangidwa post nd MikoziπΉπΈπΊππ
MSCEπ€Έπ
04/09/2025
Bwerani ku WhatsApp channel yanga ndikuzeni zambiri,link in the comment boxππ
29/08/2025
Fresh DΓΈn Abebu
Amaimba bwino nd dolo
Tamvelan izi
π₯ π
https://youtu.be/BDoxEOCi1x4
29/08/2025
https://youtu.be/Ouj4jZWI2YY?si=vc3cqrlU66mvDW3R
Now out jay twayπ₯π₯π₯
29/08/2025
Happy Birthday Giboh Pearson Phalombe Musik , Keep on working hard, hardwork sinama.
Timakufila π₯π₯
Tapangisan beat yanu lero yokoma kuimba kwa Chapter Beat's pa mtengo wadziii
#0996731555 WhatsApp or call mumvana
π₯π₯π₯
12/08/2025
Tipangen follow ku tiktok πππ
Figoh. Mw on TikTok ..mw 197 Followers, 502 Following, 14 Likes - Watch awesome short videos created by Figoh. Mw
Opportunity star β¨ β¨ waikungaso hit π ina iyi.. ππ
Tiyen ku tiktok kuli challenge ya Nyimbo imeney π₯π₯π₯π₯π
Click here to claim your Sponsored Listing.
17/07/2025