PortHerald Press

PortHerald Press

Share

20/06/2026

Big shout out to my new rising fans! Promise Wa Menas, Phillipo Chibweza, Gift Wa Benjaman Adam, Rashid Mkapa, Jeanrose Sichali, Mary Wa Leonard, Clement Marko Tayani, Lyness Wa Owen Phiri, Yvonne Malunga, Kelvin Mphero, Alinafe Kutsata, Juliet Chirwa, Prince Escales, Martha Chimaimba, Lucia Singano, Leniya Chitseko, Rixina Moyo, Mirrium Pinky Malenga, Mphepo Mphepo Chamtchanga, Alefa Kaliza, Ryashi Rayshi, Idah Mathews, Cdala Mmiriwa, Cindie Chiwacar, Digger D Wen Wen, Julias Kadenge, Greenda Samson, Triza Frackson Steble, Robert Charles, Benson Wamaule Hassan, Elyda Tanyaze Namlauzi, Bitton Mpwahiwa, Derick Mmanga Sando, Mupacho Munthali, Stiff Arsenalic Munguyi, Akondah Banda, Martha Dube Sakala, Miriam Kanjoxy, Deliwe Singini, Mpotole Wezzi, Aida Mtendere, Joana Phwandaphwanda, Elias Nkhoma, Masauko Mbvundula, Lucius Wokondeledwa Nampuluma, Hassan Sinja, Haswel Alfred Kamowa

19/06/2026

Bungwe logawa magetsi dziko muno la ESCOM lati likupitilira ndi ntchito zosintha mapolo amitengo n’kuika a simenti mpaka December chaka chino.

Malinga ndi ESCOM, ntchito imeneyi ndiyo yomwe ikuyambitsa vuto la kuthimathima kwa magetsi m’maboma a Phalombe, Thyolo ndi Mulanje.

Mkulu wa ofesi ya ESCOM ku Phalombe, Blessings Maloya, wati chifukwa cha ntchitoyi magetsi azithimitsidwa kwa maola 10 patsiku, makamaka Lamlungu ndi Lolemba sabata iliyonse.

Maloya wati cholinga cha ntchitoyi ndi kulimbikitsa kagawidwe ka magetsi komanso kuteteza zipangizo za magetsi zomwe zimagwa nthawi ya mvula ndi mphepo.

Komabe, amalonda ena ku Phalombe adandaula kuti kuthimathima kwa magetsi kukubwezera m’mbuyo mabizinesi awo.

Telephone

Website