DPP Visions
15/10/2024
President koma uyu olandira half salary pa salary yake we are missing you until you are coming back into government very soon
Koma Amalawi Mukuziwa k*t Katundu wakwera mu Chisisi? Kapena ndikubeledwa ndi ine et?
Wina akaona ngat Ku chikwawa kuli anthu osazindikira koma ai ndithu wangozindikira akumowoza, pozilimbitsa tima ati ife tinazolowera kuwowozedwa🤣🤣🤣 ok izo zili apo tisaiwale k*t pa 08:30 Brian Banda akhale akucheza ndi our expectation Professor Author Peter Mutharika.
Like Dpp visions page
After APM kucheza and providing food to the Islamic society at Liwonde and Mangochi Turn off in Balaka district, Tomorrow he expects to explain more about political issues on Times TV with Brian Banda at the time of 08:30Pm
Click here to claim your Sponsored Listing.