Frasamiez

Frasamiez

Share

17/01/2026

She said: ‘I don’t want a man controlling me, I choose single life!’
Aaaa sister 😭 relax please!
Single life but 5 boyfriends?? 🤣🤣
This one is not relationship, it’s BODMAS:
Brackets of lies, Division of time, Multiplication of men 💀💀”
🤣😂😳😂🤣😁🤣😂

10/01/2026

ZIKUOPSA KU IRAN 🇮🇷

Ogwira ntchito m’zipatala zitatu ku Iran auza BBC kuti zipatala zawo zadzaza kwambiri ndi anthu ovulala ndi mitembo, pamene ma protest otsutsa boma akupitilira mwamphamvu.
🩺 Dokotala wina ku chipatala cha ku Tehran wati:
👉🏾 “Achinyamata akuwomberedwa mwachindunji kumutu ndi ku mtima.”

Dokotala wina wanena kuti chipatala cha maso (eye hospital) mu mzindawu chalowa mu crisis mode chifukwa cha ovulala ambiri.
👩🏾‍⚕️ Ogwira ntchito awiri azachipatala ananena kuti akuchiza anthu owomberedwa ndi mfuti zenizeni komanso ma pellets, osati rubber bullets ayi.

🇺🇸 Lachisanu, USA idanenanso momveka kuti kupha otsutsa kudzayankhidwa ndi yankho la asilikali.

Kumbali ina, boma la Iran layimba mlandu USA, kunena kuti ndi yomwe ikusintha ma protest amtendere kukhala zachiwawa ndi kuwononga katundu.

🗣️ Purezidenti Donald Trump anayankha pa social media nati:
👉🏾 “Iran ikuyang’ana FREEDOM, mwina ngati kale konse. USA yakonzeka kuthandiza!!!”

09/01/2026

Let's respect that 🤣🤣🤣

Want your business to be the top-listed Media Company in Salima?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Salima
SANDTON