Walezii
4 months ago i signed a new deal ndi record ina yake yomweso muli ZONKE...we started kujambula ma projects...koma kamba ka zinthu zina UBALE Wathu tinauthesa ndipo will be working as an INDEPENDENT ARTIST.
had a chart with my bro LAY B SALIMA ndipo pamene mukudikira new music yanga tili MKATI mophikaso ina...my fans konzekani tikupanikizani.
24/10/2025
ku salima kuli anthu a LUSO ambili koma ichichi chinakunga beat imene malinga wamenya FREESTYRE ndichoopsaa...his name is Simiya ....uyuyu ndi dolo ka 100 chilandire ulemu.
12/09/2025
Mukavala mazenera maso muona k*ti ndagwera ndege,,,,,,haters will say it’s edit,,,I’m going to NAIJA to record a song with Wizkid the king of afrobeat 🙏
Click here to claim your Sponsored Listing.