Davie Jonathan

Davie Jonathan

Share

15/03/2025

FCB Nyasa Big Bullets FC(Ltd)
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή

πŸ’’πŸ’’Khaaaaa Welcome Dominic Musonda
πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯πŸ’₯

πŸ”₯πŸ”₯Nditha kukuuzani kuti pachoka mzako pali malo pomwe ThePeoplesTeam yakwanitsa kusaina katswiri osewera kumbuyo ochokera mdziko la Zambia Dominic Musonda....Dominic Musonda amasewera kumbuyo chakumanzere ndipo wasaina contract yachaka ndimgwirizano oti adzamuonjezera ngati atachita bwino chaka chimodzi chomwe amupatsa.

πŸ”₯πŸ”₯Kubwera kwa osewerayu kwathetsa nkhawa zomwe zinalipo kutsatira kukana kusaina contract kwa Alick Lungu komaso kuvulala kwa Crispin Mapemba. Musonda asanabwere ku Malawi amasewera timu ya Mutondo Stars ndipo waseweraposo timu ya Green Eagles season ya 2021/23 ndipo osewerayu wakhala sabata ziwriri akupanga mayeso ndipo Technical Panel yamupanga recomend kuti ngwabwino amupatse mpata.

πŸ’’πŸ’’Musonda akhale akunyamuka limodzi ndi anzake pomwe Bullets ikulowera chigawo chapakati kukasewera nditimu ya Kamuzu Barracks.

πŸ“’πŸ“’Ndine osangalala kwambiri kuti ndapeza mwayi otumikira timu yaikulu ngati Bullets. Ndikudziwa zoti ndikuyenera kudzimenyera nkhondo mcholinga chakuti ndizipezere malo chifukwa timuyi ili ndi osewera aluso kwmbiri choncho ndizipereka kwatunthu kuti ndizipezere malo. ""Watero Musonda atasaina contract yake ndi Bullets....

🎊🎊Welcome Dominic Musonda


πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή

14/03/2025

Please write your prediction FCB Nyasa Big Bullets

14/03/2025

2020: 🌚
2021: 🌘
2022: πŸŒ—
2023: πŸŒ–
2024: 🌝

Akazi mwationjeza tu
πŸšΆπŸ’”

22/01/2025

a.888bets.mw

Want your business to be the top-listed Clothing Store in Ntcheu?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Website

Address

Ntcheu