Yamikani Raphael Mw

Yamikani Raphael Mw

Share

27/02/2024

#

NDUNA YACHENJEZA PA NKHANI YAZIONETSERO

Nduna yamaboma ang'ono a Richard Chimwendo Banda yawuza mavenda kuti asamachite nawo zionetsero ponena kuti zimabwenza mbuyo bizinesi zawo.

Ndunayi yati anthu omwe amatsogolera zionetsero amangowagwilitsa ntchito pomwe iwo amakhala akuvutika.

"Tsegulani maso anu ndi kuona! Njira yabwino yazionetsero ndikubwera kudzatula nkhawa zanu osati kuphwanya zinthu," atero a Chimwendo Banda.

Iwo apemphanso mavendawa kuti agwilane manja ndi khonsolo ya Lilongwe pochotsa anthu omwe akugulitsa malonda mbali mwansewu.

Olemba Lucy Kadzongwe, Lilongwe.

27/02/2024

Ndinali off magets anamvuta mmmm am back online

25/02/2024

You can work for someone salary the whole month, writing reports just to safeguard his/ her Job tisafooke one day GOD will answer our tie's

Photos from Yamikani Raphael Mw's post 25/02/2024

Hundreds of people from Senior Chief Kapoloma in Machinga are today expected to receive some maize flour at Nainunje Community Ground where Machinga District Council is launching a distribution exercise meant for those affected with hunger.

The exercise follows government announcement that through the Agricultural Commercialisation Project, it has procured about 23, 000 metric tonnes of maize flour through World Food Programme in response to the hunger situation, which has affected various communities in the country.

According to Machinga disaster risk management officer, Shepherd Jere, about 48, 669 households who were drawn through the Malawi Vulnerability Assessment Committee, are expected to benefit from the exercise across the district.

Deputy director of preparedness in the Department of Disaster Management Affairs, Fedson Chikuse is presiding over the launch.

(Report by Haneeph Maulana)

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Nkhotakota?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Nkhotakota