Daily Net
21/05/2026
Mnyamata wazaka 18 dzina lake Narendra Kumar wa ku India anathamangira kuchipatala atayamba kuchepa kwambiri thupi.
Madokotala anadabwa kwambiri atamuyeza ndipo anapeza kuti mkati mwa thupi lake munali mapasa otchedwa parasitic twin, omwe anali ndi mano komanso tsitsi.
Mapasawo anasiya kukula ali akadali m’mimba mwa mayi awo ndipo anakhalabe mkati mwa thupi la Narendra kwa zaka zonse 18.
21/05/2026
Mwamuna wina ku Dowa adayitana msonkhano wa banja atapeza zoseweretsa zogonana ziwiri m’chikwama cha mkazi wake.
Anthu ena mmudzimo agawikana maganizo, ena akuti mwamunayo anapitiriza nkhaniyo mopitirira muyeso pomwe ena akuti mkaziyo analakwitsa kubisa zinthuzo.
Ayi Azimayi mukuziwa kukwiya 🙌 akuti nkhani yake bambowo anangopakula ndalama alibe nde awang'ambira malaya sangangodya katundu ulere Ayi koma bambo yo wafotokoza momveka bwino akuti anali ataledzera samaziwa chomwe akuchita.!!!
21/05/2026
Akakupeza kaya 🙌
________________
Zosayenda boma lati amene adapanga poster ndikugwilitsa ntchito dzina la Professor Arthur Peter Mutharika pamndandanda wa anthu omwe akuti atumiza mauthenga oyamikira kuti Arsenal yatenga premier league akuyenera achose, lamulo lisanamusake
Ndipo ati Purezidenti, Professor Arthur Peter Mutharika, sanatulutse uthenga woyamikira timu ya Arsenal chifukwa chopambana English Premier League ya chaka cha 2025/2026 monga momwe poster yomwe ikuyenda pa social media ikunenera.
Kutero muyenera muchose post yo lamulo lisanakusake chifukwa ndi mlandu!
[MASAPOTA A ARSENAL JIJILI JIJILI EH]
Chikondi chili ngati ukusaka Nyumba ya Rent, umayipeza ya bwino kwina utalipira kale
21/05/2026
Mkazi wina wadandaula kuti mwamuna wake samachita zachikondi pa nthawi yogonana.
Iye anati kuyambira pomwe anakwatirana, mwamuna wakeyo sanamupsompsonepo kapena kumusonyeza chikondi asanayambe kugonana. Nthawi zonse amangomuuza kuti atsegule miyendo, kenako amalowa ndi kudzikhutiritsa yekha osamuganizira.
Mkaziyo ananenanso kuti zinthu ngati kupsompsonana ndi kusonyezana chikondi n’zofunika kwambiri chifukwa zimapangitsa banja kukhala losangalala pa nkhani yogonana.
Anthu adzukira akulu awa 🙌 ati kwenikweni chawalimbitsa mtima nchani kufika pojambula akung'alura chonchi Eh!
20/05/2026
UTHENGA WOTHOKOZA 👏
From Mr and Mrs Elemiya
Okondedwa Abale ndi Alongo❤️,
Mwachimwemwe ndi mwasangala tikuthokoza nonse potengapo mbali magawo osiyanasiyana (Mapemphero, chilimbikitso komanso kupezeka kwanu) pa Ukwati Wathu womwe unaliko pa 16 May👏.
Ine ndi banja langa tikukuthokozani nonse kuchokera pansi pa mtima ndipo tikupempha Ambuye kuti abwezeretse pa zonse mwaononga pa Ukwati Wathu 🤲
Zikomo kwambiri chifukwa mwakhalanafe ndipo simunatisiye tokha mu nyengo imeneyi 👏❤️
Mwachikondi ndi Moyamika
Mr and Mrs Elemiya 🫶♥️👏
Akuti alanda zonse “Komatu anthuwa sanasiyane mwantendere chenicheni chilipo...”😄
Nkhani yaketu akuti chifukwa cha Mamuna mmodzi mpaka ndeu 🤦
20/05/2026
Mai wina wanena molimba mtima kuti ngati mwamuna wake akapita ku South Africa kokayang'a ntchito n’kumusiya ku Malawi kuno kwa zaka zambiri, sangathe kukhala yekha osachita chibwenzi ndi mwamuna wina.
Iye anati kusungulumwa komanso kusowa chikondi cha m’banja kungamupangitse kuchita chinyengo. Anawonjezera kuti ngati mwamuna wake akufuna kupita kunja atakwatirana, ayenera kumukonzera zikalata zoyendera kuti apite limodzi ku thebako.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mzuzu
MALAWI