I Cris mony intertainment
28/04/2026
get well soon madhala zeze ๐๐
chabweratu oh
04/02/2026
Nyamatayu Akuti anavara uniform ya tchemwari (dress) wake chifukwa choti iyeyo alibe uniform, aphuzitsi kuwona izi anamutulutsa , ndipo apopo azake akumuwowoza.
Zikuoneka nyamatayu Ali ndi mtima wofunitsitsa school koma mavuto sakumulora kuti izi zikhale zotheka pa moyowake.
Pamene ena akutaya nsima, ena akugona ndi njala, pamene ena mukusitha zovara kanayi pa patsiku ena akuchita kuzisowa zovara zolongosoka
Dziko ndilokondera.
04/02/2026
komatu anthu inu Anthu atutumuka ndi kanema wa CCTV ku Nairobi amene akuonesa wantchito wa m'nyumba akumuyamwitsa mwana wa abwana ake mkaka wa ngati mamina koma boys zafika apa ๐คฃ๐คฃ๐คฃ๐คฃ๐คฃ๐คฃ
01/02/2026
ndiye kuli anthu ophunzira koma ali mbuli yotheratu mawu amodzi kwa mayi ameneyi
31/01/2026
Dzaka 47 opanda mwana๐ญ๐๐๐.
Mayi wazaka 70 zakubadwa wabeleka mwana wake oyamba dzulo.
Mayiyo akuti akhala akulira pamaso pamulungu kufuna mwana, ndipo adayitenga mimba mu 2025 mpaka dzulo wamuona mwana wankazi mmanja mwake.
Mulungu ngwabwino๐
31/01/2026
mupatseni ndalama yake munthuyi ๐คฃ๐คฃ๐คฃ๐คฃ
29/01/2026
nkhani yatipeza chakumene eeeeeshy azimayi why ๐ญ๐ญZoopsatu ๐๐๐๐Mmayi ali pa chithunziyo ndi mzika ya dziko la South Africa waombera ndi kupha Mwana wa dzaka 5 ali pachithuziyo mdela la Hammaskraal mdziko la South Africa, Nkhani ikuti mwanayu amasewela ndi anzake paja pa fupi ndi nyumba ya mayiyu,
Ndiye zikumveka Kuti mmayiyu anawauza anawa Kuti akusokosa akasewere kwina, Koma anawo anangochoka kanthawi kochepa kenaka abwereranso, basi mmayiyu kungotuluka ndi mfuti ndikumuombela mwanayu emwe anafera pomwepo,
Ndiye zikumveka Kuti mwanayu Makolo ake ndi ovutikirako basitu mmayiyu kupita Kwa Makolo ake amwanayu kuwauza Kuti mukatseketsa mulandu wu ku police ndikuthandizani chilichonse mpaka Mwana wanu aikidwe mmanda,Koma Makolo wo sanalore,
dzulo mmayiyu analowa court momwe amayankha mulandu okupha, Ndipo court litamufunsa chifukwa chomwe anapangira izi iyeyo anayankha kuti iyeyo sanaombele mwanayo dala koma amawaonetsa amzake mfuti yake ya tsopano yomwe wagula ndiye mwatsoka zinapezeka anaombera mwanayo, pakanali Pano amukana bail mlandu wake ulowanso court masiku akubwerawa๐๐๐
Sidenote:Uyu afere kundende ndi oipa
28/01/2026
W@pha ana Ake omwe ๐ข๐๐ญ
Ku Kenya amayi mukuwawonawo akuti atayambana ndi mamuna wake, iye basitu anaphika phala ndikutsira poyizoni ndikuwapatsa ana Ake onse atatu ndipo anawo analandira phalaro mwachikondi ndi sangala kuti amayi amatikonda atiphikira phala zachisoni anawo atadya anagoyamba kusaza magaz! Kenakoo kuphupha ndikufera pompoo amayiwo akuwona.
Zosezi akuti anachita Ati pofuna kumukhaulitsa mamuna wake ๐ข๐ข๐ข๐
Padakali Pano zimayiyu Ali maja mwa apolice
_________
Abale mukuti ndi chani ichichii ๐ข๐ญ๐ญ
27/01/2026
STEENBERG-CAPETOWN
Mammawa omwe Uno chamma 6 ,
Anthu ena amuwombela Wina wake akugona mnyumba mwake ndipo wafelatu pompo...
Izi zachitika mu Crestway.
Click here to claim your Sponsored Listing.