Max P Spark
16/04/2026
Mtsogoleri wa chipani cha Economic Freedom Fighters EFF mdziko la South Africa Julius Malema wadzudzula yemwe amaweruza mlandu wake chifukwa cha tsankho lake.
Iye amalakhula izi ku khamu la anthu kunja kwa khothi la ling’ono la East London pambuyo pogamulidwa ndi oweruza Twanet Olivier yemwe ndi wa chizungu kuti akakhale ku ndende zaka zisanu,koma wapatsidwa belo ncholinga chokhala ndi mpata opanga apilu chigamulochi.
koma zimayi uyu simunthu ayi ndioyipa kwabasi , sankho labwanji limeneli.
fans
Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Machinga?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
http://wwwmaxpspark.com/, https://MaxPSpark.com/
Address
Machinga
98
98