Morale The Rapper

Morale The Rapper

Share

12/06/2026

Natural beauty, Nasibeko🤗
Pitani mukamwe ulionse mukufunawo Lero Friday, ndilipira ndi FaceCard🥳🌚
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

12/06/2026

Kodi mukamati "Hey Babe" ku Dm ndimakhala nnakulorelani kutiko?🤔

12/06/2026

Moti titadutsana Sungacheuke?🌚
Nena Moopa Mulungu.
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

11/06/2026

Goodnight guys, Lero musandilote ndatopa.🥱

11/06/2026

Eish, Ex wanga nde akundivutitsa bwanji, angoyimba😒

Photos from Morale The Rapper's post 11/06/2026

Ofunika new tattoo, ndiyike pati?
Kupikisana kuwala ndi Dzuwa🥱❤️
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

11/06/2026

Ok zinazo m***a kukamba Koma zoti ndine Chiphadzuwa simungatsutse🥱
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

Photos from Morale The Rapper's post 10/06/2026

Mkazi wakumaloto ako uja ndi ineyo.
Koma sindingakulore.🥱
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

10/06/2026

Pheee kuganiza kuti Nyimbo yanga yifika 50k views Koma?🤔
https://youtu.be/ZWDsr4eULx4?si=D7

09/06/2026

Ine sinnapaleko Ndipo sinzapalako🚨🎶🔥🥳Iyi yituluke liti???🔥🔥

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Lilongwe