Blessed SOULS Ministries Int.
12/07/2022
Ngakhale zinthu zitafika pothina, musalore machenjera a satana kukuiwalitsani zabwino zomwe Yehova wakukonzerani. Muzikumbukira kuti satana kwakwe ndi kuba, kupha ndi kuononga. Tsono Kodi Inu mudzapindulanji kupeza DZIKO lonse nkutaya moyo (soul) wanu (Mateyu 16:26)?
Pewani tembelero lomwe Mulungu waika Kwa onse odzigulitsa okha Kwa satana, wonyengayo ( 1 Mafumu20:21).
Mzimu woyera awalitse njira yanu kuti muzindikire machenjera a mdaniyo mdzina la Yesu. Ame.
Want your place of worship to be the top-listed Place Of Worship in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Nathenje
Lilongwe
Lilongwe