DPP PRESS
Uyuyu amatha ndipo akupanga zoopsa... Chakwera watiuza bwino
Ku Parliament kwabeba π€£π€£π€£
08/11/2025
Kumasamala poyankhula. Lero ndi izi
08/11/2025
Wisdom starts with fearing God.
A humble woman, Hon. Mary Thom Navicha today MP, Minister of Gender, Disability... God bless her and the mighty DPP π
08/11/2025
Boma la Malawi layamba ntchito yofufuza za kubedwa Kwa mafuta pafupi pafupi 30 million liters a Petrol komanso Diseal
Mchaka Cha 2023 boma la DRC linapereka mafuta okwana 27 million liters othandizira kusowa Kwa mafuta mdziko lino
Tsoka ilo bungwe la NOCMA linarandira mafuta okwana 3 million liters okha ngakhale kuti mafuta onse ku DRC anaperekedwa.
Mafutawa anafika mdziko lino pansi pa ulamuliro wa chipani cha MCP ndi utsogoleri wa Dr Lazarus Chakwera.
Bakili Muluzi TV
Pa 6 March 2024, Bakili Muluzi TV inafotokoza kuti Chakwera amasinthanitsa asilikali a Malawi Army ndi Mafuta a galimoto ku DRC.
Ena ankayesa propaganda; Lero after 20 months zayamba kuululika.
HISTORY IS THE BEST TEACHER.
*Voster C Nundwe* πΏπππ²πΌπ¦
DPP PRESS
Ikutorera zambiri zokhuza ndi
Chikumbutso Mphatso Doba
Paja mumadandaula nkhani yokhuza ma hule pa ndale
Apapa ndikhulupira mwayankhidwa
08/11/2025
Prophet Bushiri anena kuti asumira Steve Kayuni, amene anali mkulu wozenga milandu ya boma.
Iwo anene kuti pamene mwana wawo amafunika thandizo la chipatala cha kunja, Steve Kayuni, ponena kuti watumidwa ndima officials aku South Africa amatenga injunction yoletsa mwanayo kupita, zomwe zinapangitse kuti asathandizike mpaka kutisiya.
Zikuwoneka ngati mkulu Kayuni anapweteka gulu. Achisale anachita kulumbira kuti uyu yekha iwo ayi zokhululuka. Nayenso Tadikila anamumanga ali ku honey moon after ukwati wake.
Nyimbo ikhale ya Evance Meleka "Kaya ndie ukuona bwanji yemwe ukhamunyoza alipachiongolero"
http://sharevideo1.com/v/N1g2azRHX0NVYTA=?t=ytb&f=co
Chikumbutso Mphatso Doba zabwino?
http://sharevideo1.com/v/N1g2azRHX0NVYTA=?t=ytb&f=co
Chigawenga cha MCP, akuti anawauza kuti choipa chasiya kutsata Mwini
08/11/2025
Kayuni akhoza kuyamba kusosoka ndevu
Chikumbutso Mphatso Doba zabwino?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe