Labour Relations Resolution Consult
Labour Relations Resolution ndi company imene imathandiza anthu onse ogwira ntchito mu izi:kukukambirani mulandu akakuchotsani ntchito,kuwerengetsa ndalama zanu zonse(terminal benefits),kuthetsa nkhaza pa ntchito,kuonetsetsa kuti ufulu wanu sukuphwanyidwa pa ntchito,kukupezerani ntchito,kupezera mabwana anthu a ntchito.kukulemberani kalata losiyila ntchito(resgination letter).mukafuna thandizo kapena kudziwa zambiri,lankhulani ndi Mr Frank Dulli pa nambala iyi:0885556831.LRRC liwu la ogwira ntchito(the voice of workers).
Employers,why are siting there wondering where to find employees who r faithful,trusted,hard working.we know that workers u just pick on the raod hav disapointed you.Now that problem is over.come and consult LRRC and they help you.
LRRC provides experienced workers in your companies,shops,even domestic works.your problem of going and stand by the road looking for workers is over.consult LRRC.cal them now.
Click here to claim your Sponsored Listing.