Mindspark project

Mindspark project

Share

02/02/2026

Apa2 Ana ama2pn set iyi simayiziwa 😂😂
Check comments section

01/02/2026

Pena ngati Nes nes inu mukuona bwanji?

29/01/2026

Ambiri ayamba kale kuyiyankhulira akuti Madness Bola inakasayina Oyimba uyu Malonie koma izo ndizawo akambilana okha.Koma Chimfana ichi chikuswa sound osati masewela achina Driemo musamale . Follow and click the link in the commentsection to stream and download Sizinamtole by Malonie

29/01/2026

M’mene anayambila kuyenda ma show kuyimba weekend iliyonse kale kale tu Koma ma show amadzadzabe. Weekend inonso ma Blacks akukayimba ku ‘Road-Trip’ ( After Nguludi Turn Off )

29/01/2026
Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Lilongwe